Kuno ku Likuni tili ndi pempho loti atikonzere nseu kuchoka pa Thango kupita kwa Mpamba.
We citizens of Area 24 feel cheated with the way upgrading of the NCIC road to ZBS has been done. We had expected that the upgrading of the road would run from the M1 Road at NCIC passing through Area 24 Market to ZBS however the upgrading seems to have ended at Area 24 Trading Centre. Why is this the case?
Kuno ku Namiyango tati tipemphe nawo kuti atsogoleri athu akamapanga ma plan achitukuko atiganizire mbali ya nsewu kuchoka pakona pa 4 ways kudutsa pa Tondole mpaka kunsika
Monga mmene mungaonere mu chithuzi ndaika apache kagwiridwe ka ntchito pa msewu wa magalasi sikakuyenda bwino. Msweu uli mkati pokonza koma mbali yomwe agwirako kale kwaonongeka nthawi yomweyi.
Ine Aaron kuno ku Namiyango ndikuyamika Khansala athu komanso akhonsolo pa chitukuko chokonza msewu kuchoka pa weaving kuzungulira ku church cha CCAP mpaka pa Caltex.
Kuno ku Mzimba North East especially Njuyu ward miseu ili makora cha, wotivwire khansala withu
In Nkolokoti ward we are currently constructing a foot-pass bridge and we also would like to notify community members that we shall have a Healthy Week from the 3rd of July, 2017. Mbendera (Chair)
Kuno kwa Mziya Ulalo wakufumira area ya pa Napham kuluta kwa Nthonga uli makora yayi. Atikonzere chonde
Kuno kwa Chikundula ku Masasa Mzuzu tikuvutika kuoloka ka mlatho kathu matabwa anachoka
Sugzo ni mseu kuno ku Mchengautuba West, kulije mseu ukulu kufumira pa Belewa 1 kukafikira kwa Belewa 2
Ndati ndifunse nawo kuti kodi program yokonza mseu wa Chiputula wodusa pa four ways itha liti. Anthu tikudandaula kuti ukuchedwa
Mseu uli kunangika chomene pa Lunyango ku Zolozolo wets. Ma galimoto yangajumpha yayi nakuti tikusuzgika kujumphapo na walwali