Ndati ndiyamike atsogoleri athu kuno ku Area 25 Kabwabwa ward pokonza dongosolo lopala nseu wopita ku Chiuzimba
atipalireko nsewu kuchokera pa conner ya 49 mpaka pa famers world kunsungwi kuno ku 25
Kuno ku ndirande malabada atsogoleri athu alinganize dongosolo lopala nseu wochoka pa nsika suli bwino
tithokoze atsogoleri athu kuno ku Area 38 potikonzera bridge ya Chiwoko..
Ndati ndipempheko anthu aku Area 36 kuti pamene akukonza nseu wa Kandikole ena akumabweranso kuzachosa miyala ya quary kukagulisa. dera litukuka bwanji chonchi
atikonzereko nseu kuno ku bangwe wochoka pa nzikiti ku Namatapa kupita njira ya ku manda
Kuno kwa mngwangwa kwa T/A Kabudula timasowa msewu wabwino ndi chithandizo cha msika wabwino. Zikomo
tikonza mseu umenewu pempho lanu tiliona na bwana mp. P Ngoma
Ine chembekezo chaiwalika ndimakhala m'mudzi mwachankhoma ku area36. ndati ndiyamike kuti Akhasala athu AStela khumula ndi bwana MP AMasi akutithandiza pa vuto la madzi ndi misewu yomwe inali yoipa.
Area 24 mavuto ndi ambiri tiuzileni a MP zamavuto aza madzi, miseu mijigo ndinso ESCOM nkhani ya magetsi. t