In Nsanje Lalanje a SHADOW akumasiya matumba a mpunga ndi chimanga komanso zinthu zina monga bail ya zovala ndi ma T-shirt komanso nsalu Ku ma centre ena ovotera monga Khope ndi Magoti. Ku Magoti a achipani china atadziwa anapitako ndipo anamenyana dzulo. Pomwe kukhope ine ndinapitako just like Ku Magoti komwe ndapeza kuti ndi zoona. Please help. Katundu wa campaign Ali mu Malo ovotera.
Ma Shadow Khansala a zipani zina ziwiri kuno ku Kawale 2 ward pa Kaufulu center akuyima panjira kupereka ndalama kwa anthu omwe akupita kovota
Shadow wa kuno ku Rumphi Chidumba akupereka chakudya kwa aza chitetezo pa center ya Lukali
An incident has happened at Nyungwe centre in Karonga as agents of a certain shadow Member of Parliament were seen giving money to voters. As I report they are in Police custody
Some people in Rumphi have been taken to Chitimba police for soliciting and issuing out handouts to prospective voters.