Kuno ku Kasungu boma, ngozi zanjinga zikuchuluka. China mwazifukwa ndi kusasamala pa kayendedwe ka pansewu. Chonde a polisi tithandizeni.
There is inadequate supply of maize at the aforementioned satellite effective October 2019
Kuno kwa mgona pali anthu ena omwe nyumba zawo zinakokoloka ndi madzi, ena chithandizo analandira pomwe ena sanalandire
Njala yafika povuta ku balaka makamaka dela la Mfumu yaikulu Phimbi pomwe anthu anayi sabata yatha anakomoka ndi njala zomwe zapangitsa phungu wa delali Ireen Mambala kugawa chakudya kwa ena mu delali
Kuno ku Balaka Central East kagawidwe ka chimanga sikakuyenda bwino, ma khansala and akulu akulu azipani kumadera akumangoba thandizolo likabwera
Kasungu West kwa Sub-TA Mawawa, kodi boma bwanji likupereka zithu zochepa pazipangizo zomwe adalonjeza? Ndalama ya labor K50,000 sakutipatsa, ma door frame ndi mawindow sakutipatsa. kodi nanga ngongoleyi tizabweza bwanji ngati katundu wina sititenga