Government land has been given to people illegally in my area, Chisapo 2
Kwathu kuno mbali mwa nseu mulibe magetsi a MP anthu tinawauza koma mpaka lero sakuchitapo kathu
Ku Geisha masasa ward msika uli m'mbali mwa nseu tikufuna uchoke kupewa ngozi
tikulutilira kupempha muwaphalireko ku city va msika wa Geisha wadumbisane na mwenecho wa malo kuti wathu tambepo kuzenga
Pa Geisha msika uchotsedwe ndipoyipa ndimmbali mwamseu ngozi zikuchuluka ufunika pa malo abwino otakasuka
Good platform. For sure this will keep our leaders and service providers on the alert and so we can hold them accountable. But wouldn't there be an option like the way it is with phones kuti ena can view the platform in CHICHEWA
Kuno kwa mtsiliza kulibe Admarc yokhazikika tingatani kuti anthu asamakagone ku Maula Admarc?
Khansala wa dera limene ndikukhala sindikumudziwa thandizeni. kwa Phwetekere
GETO INO TIMASOWA BANK; Kodi Ife Kwamtsiliza Kno Sitifunika Kukhala Ndi Bank? Ndine MD Signwriter
zikomo kwambiri a-Mzinda chifukwa chopereka mwayi woti titha kumalemba ma uthenga pa mavuto akudera
Kuno ku NANKHAKA WARD Tikukumba Dam under MASAF 4 LDF project. Tiweta nsomba ndi kulima mbeu zanthilira.Timafuna mutabwela pa 2/09/16 pamwambo woyamba ntchito imeneyi. Nankhaka ward Cllr WILBES KAPIZA