COUNCILLOR chilomon ward mseu wa kwa nthukwa ukufunika phula
Kuno ku Dedza North west constituency-Magomero . MP wathu Alekeni Menyani uthenga uwu umufike: Nseu kuchoka pa ndyampho bridge kukafika pa Lobi suli bwino komanso pa Mbazi school abweretse ma desk. ine Simon Jovinal carpenter
tati uthenga uwafikire bwana khansala ndi bamboo MP atikonsere nseu kuno ku Gologota Area 23 pafupi ndi nyumba ya kantwanje. Komanso ku Kaliyeka Chipasula kukafikira pa msika nsewu suli bwino. Brian Samute telela wa chinyamata
atsogoleri athu chonde tikonzereni nseu wachoka pa stage ya SDA kupita ku ntunda kuno ku Kawale 2
kuno ku Kawale 1 nseu wa ku Block A kuchoka pa Banja la mtsogolo sulibwino . ukakhala chomwechi ikabwera mvula pavuta
kuno kwa biwi patsogolo pa 3 ways pali Gonjetso shop nseu sulibwino akonze
Kuno kwa T/A Makata ku Blantyre, bridge ya pa mtsinje wa Mlombozi inakokoloka chaka chatha,koma mpakana pano sunakonzedwe. Tiyembekezere kuti ukonzedwa liti,chifukwa nyengo yamvula ndiye yafikana
Kuno ku Kawale 1 nseu wochoka pa banja la mtsogolo si ulibwino. chonde atikonzere
Kuno ku Mtandire tikupempha atsogoleri athu kuti achite chotheka atikonzere nseu. bwanji anzathu kumadera ngati ku 25 ndi ku 36 akuwapalira mseu ife ayi
Tati tipempheko kuti atithandize ndi mlatho kuno ku Solzbery lines mzuzu