Ife tinene zaku 36 Phwetekere ward msewu nde uli bwino koma nkhani yina cha nkati kwa chumba atikonzere mlatho pa Nsambeta
chitawira bwana MP akonze mlatho wa pa mlambalala kupita ku ntonya
khansala wathu ku Ngwenya adalonjeza mseu sukukonzedwa mpaka pano
Ku Chinsapo 2 atikonzere nseu wopita ku Kakule primary school. Mayi Loga. Business Woman
Residents of SESE ward in Lilongwe are today fixing rings at Tongole Bridge in the area. Councilor for the area Frank Lebian says they will also do the same in nsinje and mchitanjiru areas in the ward. Share with MZINDA a report on developments in your area
Bwana MP kuno ku Bangwe athire dothi nseu wochoka mutala kupita pa Nazarene. SAULOS WOMETA
Kuno ku salima msewu wathu sulibwino,okumbika komaso ndiwaung'ono kuchokera ku salima depot kupita ku sengabay Livingstonia,road signs ulibe koma ndiomwe umakhala busy nthawi zonse.tithandizeni pliz.Ine Richard katengeza,ngolowindo village,TA maganga
Kuno ku Area 23 bwana MP ationereko nseu wopita ku Don Bosco.. tikuthokoza adathira miyara malo ena koma ena sadathire. tikuopa kuti nthawi ya mvula ikafika nseu uzavuta
Kuno ku Mulanje Mimosa. Pempho ndi loti atipalire mseu kuchoka pa Mimosa kufika pa msika wa Chikuse. Mayendedwe monga kwa anthu ochoka kwa Nkhonya amavutika.
area 36 nseu wochoka pa mbukwa kupita pa tank akonze. wakumbika kwambiri
Kuno kwa Senti tikupempha kudzera mwa Khansala wathu kuti atikonzere mlatho wopita pa Mkombaphala