Tati tipemphe nawo kudzera pa Mzinda kuti atithandize kuno kwa Jokala ku Zomba, nkhani ya mseu, mseu wathu kuno sulibwino. Matias Kalemba
In Kasungu, there is this growth of unruly behaviour of minibus touts who sometimes damage properties of passengers in a quest to force them board the minibus they are touting on. Its high time police dealt with this unruly behaviour as it inconveniences the passengers.
Kuno kukasungu boma T/A kaomba, anjinga za moto samayenda bwino komanso opanda zida zowaloreza kuyenda pa nsewu .. Chonde Apoli tithandizeni.
The bridge at Lingadzi near sanctuary has been washed away by flood water
On the high way to Limbe we have floods on the road and we request your assistance as traffic cant move.
There is a drainage blockage along along stella maris secondary school
vuto la nseu kuno ku ngerenge karonga. wadyeka kwambiri magalimoto akulephera kudusa
Ine ndimakhala ku zingwangwa ku BT, ndimati ndidandaule miseu yathu mu dela limeneli siili bwino. Maenje maenje ndithu ndiye madzi a mvula akumadikha mmenemu, sizili bwino ndithu
Kuno ku Kasungu msewu womwe unaonongeka ma yenje ayamba kuukonza
Kuno kwathu program yokonza miseu yidaimila panjira monga mseu wa kwa Senya to Chitete river ndi Kapindula to Chitete. Sitikudziwa kuti asembule ma plan awo ndiotani