Kuno kwa T/A Makata ku Blantyre, bridge ya pa mtsinje wa Mlombozi inakokoloka chaka chatha,koma mpakana pano sunakonzedwe. Tiyembekezere kuti ukonzedwa liti,chifukwa nyengo yamvula ndiye yafikana
I would like to report issues of power blackout in my area at Biwi.We have had no power this whole weekend.
Ndati ndiyamikire Khansala wa Mbidzi ward Mike Chimzukira chifukwa choika ma bin mu malo ambiri ku old town kuti ukhondo upite patsogolo. anthu nafe pa ife tokha titengepo gawo. Zelesi Kathumba wa zikwama
area 23 tsabango 1 kuli vuto akuzimazima kwa magetsi please help us
ine dzina langa Ofesi ndimagwira ngati guard pa Kanjala motors vuto liliko kuno ku Chilinde ndi madzi. pilizi chonde zithe
kuno ku Chilinde 2 cha kwa Sankhawekha magetsi akuyenjeza. amuna anga amapanga zootcherera moti pano kapezedwe ka ndalama kakuvuta. Mayi Sakwata
kuno ku Mchesi madzi akuvuta kwambiri, ine monga m,modzi mwa osewera mpira mu timu ya Bekery zikumandivuta kusamba tikachoka kusewera mpira titada koma kupeza madzi asiya
I humbly request the Lilongwe city council to please come and empty the waste dustbin at Mchesi market. Waste is overflowing
Kuno ku Chilinde 1 pempho lathu ndi lakuti amange ma toilet pa msika. inde zinyalala amazachotsa komabe tiketi yomwe timadula athaso kutikonzera ma toilet akhonsolo
kuno Ku area23 tsabango 1 kuli vuto lakut pamanda agologota mbalimbali mwamanda akumatayamo zinyalala nde awonepo
Tuesday night electricity units ran out around 11pm so we were in black out. The next day we went to buy units. We put the units in the meter and it just keeps saying 00. Last night we then drove to Kanengo to the escom faults office but were not helped. Today we are still without electricity. Mpaka we had to ask our neighbour to keep our relish in fear of it going bad. We just called the faults office in kanengo to let them know they should send assistance so we are still waiting.
Thanks for your notification (about engaging Chibuku on sanitation) but i have already engaged them to do as said. Once again thank u keep on updating me. Gibson Nyirenda - Councillor Chilinde II
Would our Councilor for Chilinde 2 please take up the issue of sanitation with Chibuku officilas because their people working at Chikwaye tarven are just dumping waste anyhow
Here in Kawale 1 our request is that our councilor should engage the city council so that the waste removal service should also be collecting waste accumulating at the Health centre
atsogoleri athu chonde tikonzereni nseu wachoka pa stage ya SDA kupita ku ntunda kuno ku Kawale 2