Suzgo ni madzi akumwa kuno ku Geisha timatunga pa kachitsime koti sikasamalika
Kuno ku Masasa maji ayo tikumwa yali makora yaye. watowvire na Mjigo please
Kuno kumasasa vuto ndi madzi. madzi abwino a-Water board sanabwere komanso mjigo kulibe timatunga pa ka chitsime kosakhala bwino
Kuno ku Masasa suzgo ilo tili nalo ni magi. please chonde watiwvire
Kuno Ku Njelenje Akhasala mlatho Kulibe atiganire akamapempha ndalama ya chitukuko
Tati tiwakumbutse atsogoleri athu kuti Zolozolo clinic mpaka pano sitikumvako kalikonse kuti itha liti. kodi kapena ndalama sizidayende bwino
Kuno ku Mtandire tikupempha atsogoleri athu kuti achite chotheka atikonzere nseu. bwanji anzathu kumadera ngati ku 25 ndi ku 36 akuwapalira mseu ife ayi
While it is appreciated that the whole country is experiencing load shedding, the scale of load shedding in area 47 is just too much. I would urge 'equitable distribution; of load shedding with other areas.
Water rationing schedule week beginning 14th November, 2016. Remember: Always use a bucket, pail, cup, NOT running water to wash clothes, utensils and brush teeth.
Kuno ku Mtandire kwayamba mapokoso pankhani ya Admarc, pamalo pomwe akufuna kuyika akhansala, Azimayi amagwirapo ntchito yosamala ana amasiye. Chonde amabungwe iwafikire nkhaniyi alowererepo kuonetsetsa kuti zokhumba zandale zisasokoneze njira zina zomwe ena akuthandizikira kudera
I would like to agree with what the councilor that was featured in the Mzinda radio program today said about the lack of a good working relationship between our leaders being a cause for lack of development in some areas. this is happening especially where the MP and Councilor belong to different parties. perhaps Councilors should not stand on a party ticket. S. Soko. Nancholi
Kuno ku likuni tanyadila Magetsi ayaka dzulo komaso lero anangothima masana Mphatso
Ndati ndipempheko kuti ngati kuli kotheka mabungwe omwe mukupanga za Mzinda mutifikireko ife akumadera ena monga kuno ku Matawale
Kuno kumasasa suzgo ni mabridge yanyake yali kunangika