Bin yathu kuno ku NAYIZI pa Msika yadzadza, chonde abwere kudzachotsa
I would like to commend ESCOM for the improvement in power supply here in Area 23. Great work team ESCOM.
kuno ku 23, dera la gologota, madzi akuvuta kwambiri, akumatuluka kamodzi kapena kawiri pa sabata.
Ife Kuno Kuchikwawa T/A Chapananga V/G Lackson Mudera Mwathu Magetsi Alipo ndipo amayaka bwino Ine F.Stephano.
There is an accumulation of waste at Mwansambo Trading. The picture shows our worst disposal pit, it is very close to main road just as you seen students are passing by. The Assembly needs to do something about this
Let me commend our Councilor for Misesa ward Louis Ngalande for being part of the big walk organized to raise awareness on the importance of planting trees. This is a welcome initiative.
My name is Peter Kamama,from Khama Machinjiri, I would like to report that our biggest problem is power. We usually have supply only thrice a week.
Kuno ku chilomon tili ndi vuto lophulika phulika kwa ma pipe zomwe zikupangitsa kuti mazi azisowa
Kuno ku Zingwangwa anthu tikuchulutsa umve kutaya zinyalala paliponse. Chonde tatiyeni tisinthe. Ine Saidi
Pa Msika waukulu ku Mbayani palibe Bin. Kotero anthu ena amakataya zinyalala ku njanji komanso malo ena zomwe zimaika chiophyezo pa miyoyo yathu
Kuno ku Zomba kwa Mpondabwino tili ndi vuto lakuzimazima kwa magetsi. Ine Lemusi Kawanga
Kuno Ku Mbayani, Pa Chipatala Chathu Pali Vuto Loti Mma Week End Sipagwilidwa Ntchito Molongosoka, Mwa Chitsanzo Munthu Ngati Wadwara Loweruka Madzulo Uyembekezere Kuthandizidwa Loremba.Tithandizeni Vuto Limeneri. Ine Stan Kazoma.
Zinyalala anthu angotaila paliponse kuno ku Mbayani chifukwa pa Msika wathu waukulu palibe Bin.AGATHA PADDY
Magesi akuvuta kwambiri kuno ku Mbayani. Ndine ulemu majiga
Ine monga m'modzi mwa kholo lomwe lili ndi mwana wa sukulu pa Nkolokoti ndati ndiyamikire khama la aziphunzitsi apa sukuluyi