Zinandisangalatsa kuwona a city akudzatenga zinyalala mudela lathu izi ndi zithu zabwino ndipo mupitilize a city koma pa msika wa old gualiver pali zinyalala ndipo sipawoneka bwino komaso pamanunkha chonde mudzatiwoneleko kuno ku gualiver, area 49.
Kuno kwa Centi zinyalala timangotaya paliponse, penpho langa nali, tiyesese pa tokha ngati anthu amudera kutaya zinyalala mosamala
Chigalimoto sichifikadi kuzaola zinyalala chifukwa nsika wa Mtandire amapanga collection ya ma market fees okha.Pano pali kukambirana kuti City Council izitolela yokha ma fees pambuyo pake chigalimoto chizibwera. A Soko. Cllr Mtandile Ward
Kudos to Lilongwe City Council for stepping up efforts to keep the city clean
Along Paul kagame road on the turn to Shire building there is a sory sight of waste. is it a problem of improper dumping of waste or non collection of refuse
Umve pa mzuzu health centre kod antchito akugwira ntchito yanji makamaka ku ma toilet kukuwonjeza umve wake ndalama za boma zikupita kut?
Thank you to those responsible for clearing waste that had been accumulating at Zingwangwa market.
Pali vuto kuno kundilande'pa brige yapazambiya padzadza zinyalara-chonde tinthandinzeni.
kuno ku msika wa ndirande zinyalala ziri pali ponse.Akhonsolo achitepo kanthu.
Would our Councilor for Chilinde 2 please take up the issue of sanitation with Chibuku officilas because their people working at Chikwaye tarven are just dumping waste anyhow
Kuno ku Chilinde 1 pempho lathu ndi lakuti amange ma toilet pa msika. inde zinyalala amazachotsa komabe tiketi yomwe timadula athaso kutikonzera ma toilet akhonsolo
Here in Kawale 1 our request is that our councilor should engage the city council so that the waste removal service should also be collecting waste accumulating at the Health centre