kuno ku Bangwe vuto linali kuthima kwa magesi koma sabata yathayi zinali bwino
Kuno ku Namiyango area ya cha pa Tondole magesi akumavuta kwambiri
Tati tidandaule nkupanga report kuti kuno ku Ndirande vuto lakuzimazima kwa magetsi likupitirira. chonde atithandize.
I would like to report that the main problems that we experience here in Chilomoni are water and electricity. service delivery in these two ares is not so good
Magesi akuvuta kwambiri kuno ku Mbayani. Ndine ulemu majiga
Kuno ku Zomba kwa Mpondabwino tili ndi vuto lakuzimazima kwa magetsi. Ine Lemusi Kawanga
My name is Peter Kamama,from Khama Machinjiri, I would like to report that our biggest problem is power. We usually have supply only thrice a week.
Ife Kuno Kuchikwawa T/A Chapananga V/G Lackson Mudera Mwathu Magetsi Alipo ndipo amayaka bwino Ine F.Stephano.
I would like to commend ESCOM for the improvement in power supply here in Area 23. Great work team ESCOM.
Ine ndi Irvin Chadeka kuno ku Area 25 sector 7, ndati ndiyamikire ESCOM chifukwa cha kayakidwe ka magetsi kuchokera mid January kufikira pano magetsi akuyaka bwino kulekana ndi kale pomwe amazimazima.