Kuno ku Area 25 magetsi akuzimazima mutithandize. Mayi Chanache
Uthenga ufikileko ESCOM, magetsi Akungozimazima. Ndine Charity Kuchokera Ku Area 25 Sector 7
Kuno kwatsiliza kulivuto lakuzimazima kwa magetsi ndine harry chalanda
Kuno kwa MtsiliLza kuli vuto lakuzimazima kwamagetsi ndine harry chalanda
magets akuyenera kumayaka nthawi yayitali kumazima nthawi yayifupi mwandimva kuno ku 25
Kuno ku area24 magetsi ndi chifukwa chani amazima mammawa kwambiri anthu tikukonzeka za kutchito ndi ku school
I would like to commend ESCOM for the consistent supply of power in Chilinde newlines. Ever since I moved in about a month ago magetsi sanazimeko. I can only hope the same would be realized ku madera ena.
magetsi akuyaka moyenera kuno ku Dzenza sakudandaulitsa kwenikweni akuyesesa nsanamepo apa.
kuno ku Chilomoni Mulunguzi,magetsi azima dzulo pa 3 October m'mawa mpaka pano lero sakuyaka,tithandizeni
Magetsi kuno ku Chitedze-Lilongwe awonjeza kuzima
In as much as we understand the challenges our service providers may be facing but with regards electricity I would say we have reached our lowest point as a country. in Area 25 we are at times only having power for 5 hours in a day and at night for that matter when we have to rest and be sleeping. Please ESCOM assist us, last time I heard about the possibility of tapping power from Mozambique where are we with this.
Kuno ku Area 49 nkhani ya kuzima kwa magetis yafika pena, amayaka usiku 10 koloko nkuzimasa m'mawa 5 koloko. nde pamenepa amati ife tigwritse ntchito magetsi nthawi yanji ?