Zolozolo east pliz assist us mr MP, the health centre project is not starting as promised.
Ndati ndipemphe nawo kuti boma lichitepo kanthu kuonesesa kuti zida zina zokwaniritsa kugwira ntchito bwino pa chipatala zizipezekaso mu ma health centre. chitsanzo pa health centre ya Area 25 palibe makina ounikira muthupi aja amati Scan. nde kuti tiziti Lilongwe yense aziti mupite ku Central??
Ine mai Mwale kuchokera kuno ku Ntchisi ndati ndiyamike pa chithandizo chomwe tidalandira ku chipatala cha Kamuzu komwe ndakhalako ndi mwana wanga yemwe adali ndi chotupa, lero atitulutsa ndipo madokotala ntchito ayigwira yabwino
Ine monga m'modzi mwa anthu okhala kuno ku Zolozolo East ndati ndikambepo mobwereza kuti papita nthawi pamene ntchito yomalizitsa kumanga health centre idayima. Tikufuna Khansala wathu komanso aKhonsolo ya Mzuzu adziwe kuti Health Centre imeneyi itha kutithandiza kwambiri kotero kuchedwa koti iyambe kugwira ntchito tikumva nako kuwawa
Am a young man living here in Bangwe.My concern is the lack of sufficient health personnel at Bangwe health center. I also would like to say I am one of the youth who has the willingness to work with our leaders towards development. Let them contact us.
Pa Makhetha clinic tati tipemphe nawo kuti atikonzere ma Toilet, anadilizika
Kuno Ku Mbayani, Pa Chipatala Chathu Pali Vuto Loti Mma Week End Sipagwilidwa Ntchito Molongosoka, Mwa Chitsanzo Munthu Ngati Wadwara Loweruka Madzulo Uyembekezere Kuthandizidwa Loremba.Tithandizeni Vuto Limeneri. Ine Stan Kazoma.
I would like to send out a request to the Ministry of Health and any well wishers that there is an urgent need for a resuscitation machine at Zingwangwa Health Centre.
Tuwonga chomene a councillor withu pakutizengera admarc kuno Ku zolozolo east ward kweni tiliso na fumbo kuti ka chipatala chijulikenge pa uli.
Kuno ku chiputula ward ku Mzuzu tukhumba kuti watipe clinic. Kwa sono wanthu wakwenda long distances kuluta ku boma mwakuti ma referral tupangira pa CBO
I would like to request through our councillor and for the attention of all those responsible that they should considered giving us residents of chiputula a small community clinic. Right now people travel long distances to the main Mzuzu hospital