BOQ ya toilet

Location: Mzuzu 24-May-2023 | 09:36

Nkhani ya BOQ ya toilet ya 20 Million Kwacha Ineyo ndayimvetsetsa. Panopa ndaona kuti Khonsolo siyinapereke ndalama yiliyonse pa Toilet yimene yikutvhulidwayi. Tithokoze a Komiti pamodzi ndi Khonsolo ya Mzuzu pokambila nkhanizi ndipo zatha bwino. Tiyeni tilunjile pachitukuko tsopano. Izi zatha. Komabe a Khonsolo mutiuza liti za mtengo weni weni wa Chimbudzi chomene chikutchulidwachi?

View Details

Kusowa kwa ambulance ya ku Nalunga

Location: Dowa 27-Apr-2023 | 11:12

Kodi ambulance yomwe inapelekedwa pa nalunga hearth center a yichotsapo ndindani

View Details

Kukumba Mjigo

Location: Dowa 27-Apr-2023 | 11:08

Mjigo wa kwa MATOLANI sunakumbidwe mpaka pano chifukwa chiyani? ine D KATAMANDA VDC chair (ngozi vdc)

View Details