24-May-2023 | 09:36
  • By : +265888554471
  • |
  • 1 replies

BOQ ya toilet

Nkhani ya BOQ ya toilet ya 20 Million Kwacha Ineyo ndayimvetsetsa. Panopa ndaona kuti Khonsolo siyinapereke ndalama yiliyonse pa Toilet yimene yikutvhulidwayi. Tithokoze a Komiti pamodzi ndi Khonsolo ya Mzuzu pokambila nkhanizi ndipo zatha bwino. Tiyeni tilunjile pachitukuko tsopano. Izi zatha. Komabe a Khonsolo mutiuza liti za mtengo weni weni wa Chimbudzi chomene chikutchulidwachi?

Replies

Mzuzu Council Admin
24-May-2023 | 09:45

we are working on that

Leave A Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked*