Showing Reports From Feb 17, 2016 to Aug 15, 2020 Change Date Range

Or choose your own date range:

From: To: Go
36-40 of 745 Reports

Kuno ku Likoma Okalamba Sakuthandizidwa Bwino 0 Verified

07:10 Jun 23, 2020

Ku Likoma pa centre ya Fisheries okalamba sakuthandizidwa bwino, akumawayendetsa malo okwera ama stepe More Information » « Less Information

Likoma

Ngalande za pa msika waukulu wa Kasungu

Categories

WASH

Ngalande za pa msika waukulu wa Kasungu 27 Verified

11:52 Feb 24, 2020

Ngalande za pa msika waukulu wa Kasungu ndi zosafukula zomwe zikuchititsa kuti madzi adzilowa mu msika chonde atithandize More Information » « Less Information

Kasungu

Pempho La Bin Ku Zolozolo 1 Verified

07:31 Feb 22, 2020

Ndati ndipemphe nawo chithandizo choti khonsolo itibweresere bin yayikulu pa msika wa Apostolic. Malowa akubweresa chiophyezo cha matenda chifukwa... More Information » « Less Information

Mzuzu

Vuto La Mlatho Nkhonde Ward 1 Verified

11:39 Feb 21, 2020

Kuno ku Nkhonde ward ku Balaka. Tinapempha MP athu kuti atikhonzere mlatho omwe unasuntha chifukwa cha mvula ya chaka chatha koma mpaka lero... More Information » « Less Information

Balaka

Questions on Road Maintenance 0 Verified

06:14 Feb 20, 2020

There is a concrete carvet on Chinunu Lupembe feeder road that was meant to be completed in 2017 and we learnt that the contractor was paid... More Information » « Less Information

Karonga

36-40 of 745 Reports
Total Reports Avg Reports Per Day % Verified
745 0.45 99.73%