Showing Reports From Feb 17, 2016 to Jun 05, 2020 Change Date Range

Or choose your own date range:

From: To: Go
701-705 of 709 Reports

maji tukhumba mijiGo

Categories

Water

maji tukhumba mijiGo 0 Verified

13:18 Apr 12, 2016

Kwithu kuno pa Luzi Maji yakusuzga chomene More Information » « Less Information

Rumphi, Northern, Malawi

Bridge yinakokoloka

Categories

Roads

Bridge yinakokoloka 0 Verified

13:12 Apr 12, 2016

kuno kwathu ku chingale Zomba mlatho unakokoloka a MP anthu sitinawauze chifukwa amafika kuno nthawi ya campaign ... pano amakhala ku town... More Information » « Less Information

Zomba, Southern, Malawi

magetsi amu nsewu

Categories

Other

magetsi amu nsewu 1 Verified

13:04 Apr 12, 2016

Kwathu kuno mbali mwa nseu mulibe magetsi a MP anthu tinawauza koma mpaka lero sakuchitapo kathu More Information » « Less Information

Mzimba, Northern, Malawi

Nseu ku kasungu

Categories

Roads

Nseu ku kasungu 0 Verified

12:42 Apr 12, 2016

Nseu wa ku ma puloti suli bwino kukagwa mvula timavutika chifukwa cha matope ma galimoto amavutika kuyenda, nazo njinga sitimayendesa chifuka... More Information » « Less Information

Kasungu, Central, Malawi

Magetsi khatabay 0 Verified

12:35 Apr 12, 2016

Kwathu kuno magetsi sakuyaka tikutha 1 week pano wopanda magetsi kuwauza a-Escom faults anangoti amva pali vuto la transformer. More Information » « Less Information

Nkhata Bay, Northern, Malawi

701-705 of 709 Reports
Total Reports Avg Reports Per Day % Verified
709 0.45 99.72%