Showing Reports From Feb 17, 2016 to Dec 06, 2019 Change Date Range

Or choose your own date range:

From: To: Go
651-655 of 661 Reports

Police station yotithandiza kulibe

Categories

Security

Police station yotithandiza kulibe 1 Verified

13:29 Apr 12, 2016

Kwathu kuno katundu akubedwa.. anthu akuphedwa paliibe chabwino kukacha timamva nkhani za chisoni ........ a MP anthu tinawafotokozela kuti... More Information » « Less Information

Balaka, Southern, Malawi

chipatala kulibe

Categories

Health

chipatala kulibe 0 Verified

13:23 Apr 12, 2016

kuno kwathu ku Chiradzulu kwa pelembe dera lonse kuchoka mbali ya kwa mpama kulibe chipatala tikadwala timayenda kukafika ku chipatala chachikulu More Information » « Less Information

Chiradzulu, Southern, Malawi

maji tukhumba mijiGo

Categories

Water

maji tukhumba mijiGo 0 Verified

13:18 Apr 12, 2016

Kwithu kuno pa Luzi Maji yakusuzga chomene More Information » « Less Information

Rumphi, Northern, Malawi

Bridge yinakokoloka

Categories

Roads

Bridge yinakokoloka 0 Verified

13:12 Apr 12, 2016

kuno kwathu ku chingale Zomba mlatho unakokoloka a MP anthu sitinawauze chifukwa amafika kuno nthawi ya campaign ... pano amakhala ku town... More Information » « Less Information

Zomba, Southern, Malawi

magetsi amu nsewu

Categories

Other

magetsi amu nsewu 1 Verified

13:04 Apr 12, 2016

Kwathu kuno mbali mwa nseu mulibe magetsi a MP anthu tinawauza koma mpaka lero sakuchitapo kathu More Information » « Less Information

Mzimba, Northern, Malawi

651-655 of 661 Reports
Total Reports Avg Reports Per Day % Verified
661 0.48 99.7%