Showing Reports From Feb 17, 2016 to Apr 13, 2021 Change Date Range
Or choose your own date range:
Categories
Healthchipatala kulibe 0 Verified
13:23 Apr 12, 2016
kuno kwathu ku Chiradzulu kwa pelembe dera lonse kuchoka mbali ya kwa mpama kulibe chipatala tikadwala timayenda kukafika ku chipatala chachikulu
More Information »
« Less Information
Categories
Watermaji tukhumba mijiGo 0 Verified
13:18 Apr 12, 2016
Kwithu kuno pa Luzi Maji yakusuzga chomene
More Information »
« Less Information
Categories
RoadsBridge yinakokoloka 0 Verified
13:12 Apr 12, 2016
kuno kwathu ku chingale Zomba mlatho unakokoloka a MP anthu sitinawauze chifukwa amafika kuno nthawi ya campaign ... pano amakhala ku town...
More Information »
« Less Information
Categories
Othermagetsi amu nsewu 1 Verified
13:04 Apr 12, 2016
Kwathu kuno mbali mwa nseu mulibe magetsi a MP anthu tinawauza koma mpaka lero sakuchitapo kathu
More Information »
« Less Information
Categories
RoadsNseu ku kasungu 0 Verified
12:42 Apr 12, 2016
Nseu wa ku ma puloti suli bwino kukagwa mvula timavutika chifukwa cha matope ma galimoto amavutika kuyenda, nazo njinga sitimayendesa chifuka...
More Information »
« Less Information
Category(Pick your categories and click Go to reports )
- All Categories 745
- WASH124
- Social Protection8
- Health45
- Local Governance7
- Peace Building0
- Education17
- Roads147
- Electricity125
- Water145
- Security25
- Elections90
- Hate Speech2
- Violent Clashes8
- Pulling Down Flags2
- Handouts5
- Buying Voting Cards5
- Personnel10
- Vote Counting10
- Time6
- Barred from hosting a rally6
- Voting Materials13
- Other Elections Related Reports23
- Other64
Total Reports | Avg Reports Per Day | % Verified |
---|---|---|
745 | 0.4 | 99.73% |