Showing Reports From Feb 17, 2016 to Aug 15, 2020 Change Date Range

Or choose your own date range:

From: To: Go
646-650 of 745 Reports

Kwa Senti Atikonzere Mlatho

Categories

Roads

Kwa Senti Atikonzere Mlatho 0 Verified

11:24 Aug 19, 2016

Kuno kwa Senti tikupempha kudzera mwa Khansala wathu kuti atikonzere mlatho wopita pa Mkombaphala More Information » « Less Information

Lilongwe, Malawi

Ukhondo Ndi Watonse Mudera

Categories

WASH

Ukhondo Ndi Watonse Mudera 0 Verified

10:48 Aug 19, 2016

Ndati ndinenepo kuti Kusoweka kwa ukhondo mu madera athu pena nchifukwa choti ife anthu eni ake sitifuna kutengapo mbali. Sinkhani yomangonena... More Information » « Less Information

Lilongwe, Central Region, Malawi

Achite Machawi Pokonza Miseu

Categories

Roads

Achite Machawi Pokonza Miseu 0 Verified

10:22 Aug 19, 2016

Kuno kwa Mtsiliza tiyamike dongosolo loika ma ring mu miseu koma pakufunika madera onse zitheke nthawi ya mvula isadafike More Information » « Less Information

Lilongwe, Malawi

Kuzimazima kwa Magetsi Area 25 Sector 7 0 Verified

10:11 Aug 19, 2016

Uthenga ufikileko ESCOM, magetsi Akungozimazima. Ndine Charity Kuchokera Ku Area 25 Sector 7 More Information » « Less Information

Lilongwe, Malawi

AREA 25 Magetsi akuzimazima 0 Verified

10:05 Aug 19, 2016

Kuno ku Area 25 magetsi akuzimazima mutithandize. Mayi Chanache More Information » « Less Information

Lilongwe, Malawi

646-650 of 745 Reports
Total Reports Avg Reports Per Day % Verified
745 0.45 99.73%