Showing Reports From Feb 17, 2016 to Nov 12, 2019 Change Date Range

Or choose your own date range:

From: To: Go
641-645 of 647 Reports

magetsi amu nsewu

Categories

Other

magetsi amu nsewu 1 Verified

13:04 Apr 12, 2016

Kwathu kuno mbali mwa nseu mulibe magetsi a MP anthu tinawauza koma mpaka lero sakuchitapo kathu More Information » « Less Information

Mzimba, Northern, Malawi

Nseu ku kasungu

Categories

Roads

Nseu ku kasungu 0 Verified

12:42 Apr 12, 2016

Nseu wa ku ma puloti suli bwino kukagwa mvula timavutika chifukwa cha matope ma galimoto amavutika kuyenda, nazo njinga sitimayendesa chifuka... More Information » « Less Information

Kasungu, Central, Malawi

Magetsi khatabay 0 Verified

12:35 Apr 12, 2016

Kwathu kuno magetsi sakuyaka tikutha 1 week pano wopanda magetsi kuwauza a-Escom faults anangoti amva pali vuto la transformer. More Information » « Less Information

Nkhata Bay, Northern, Malawi

Madzi Akusiyasiya Ku Bangwe Namatapa

Categories

Water

Madzi Akusiyasiya Ku Bangwe Namatapa 0 Verified

12:18 Apr 12, 2016

ku bangwe madzi akuvuta mwezi uno wachitatu tidaona kuti patokha mpovuta kepereka dandaulo ku Water Board nde tidakamba ndi bwana MP anangoti... More Information » « Less Information

Blantyre, Southern, Malawi

Miseu Kwa m'baluku

Categories

Roads

Miseu Kwa m'baluku 366 Verified

21:38 Apr 06, 2016

Kuno kwathu miseu silibwino. tufuna langizo kuti tingasate bwino m'mene ndalama zokonzera mseu zidagwirira ntchito More Information » « Less Information

mangochi

641-645 of 647 Reports
Total Reports Avg Reports Per Day % Verified
647 0.47 99.69%