Showing Reports From Feb 17, 2016 to Jun 02, 2020 Change Date Range

Or choose your own date range:

From: To: Go
11-15 of 709 Reports

Funso pa za tsiku lotsegulira Chipatala

Categories

Health

Funso pa za tsiku lotsegulira Chipatala 0 Verified

08:33 Feb 07, 2020

Chipatala cha Mwima chatha zaka 17 koma osachitsegulila. Anthu adandaula koma kuli zii More Information » « Less Information

Balaka

Kusowa Kwa Ma Toilet Abwino M'misika

Categories

WASH

Kusowa Kwa Ma Toilet Abwino M'misika 1 Verified

07:44 Feb 06, 2020

Kuno ku Kasungu misika yambiri ing'onoing'ono mulibe ma toilet koma ma tiketi timaduladaily. Kodi ndalamazo zimagwira ntchito yanji More Information » « Less Information

Kasungu

Kufunikira kwa Ngalande ku Kasungu

Categories

WASH

Kufunikira kwa Ngalande ku Kasungu 0 Verified

10:48 Feb 05, 2020

Ngalande za mu msika ndi zosafukula kuno ku Kasungu chinthu chomwe chikupangisa kuti madzi azilowa pamalo ogulitsira malonda More Information » « Less Information

Kasungu

Mutiunikire Za Malata Subsidy 0 Verified

08:16 Feb 05, 2020

Kasungu West kwa Sub-TA Mawawa, kodi boma bwanji likupereka zithu zochepa pazipangizo zomwe adalonjeza? Ndalama ya labor K50,000 sakutipatsa,... More Information » « Less Information

Kasungu

Poor roads

Categories

Roads

Poor roads 2 Verified

08:53 Jan 24, 2020

Ine ndimakhala ku zingwangwa ku BT, ndimati ndidandaule miseu yathu mu dela limeneli siili bwino. Maenje maenje ndithu ndiye madzi a mvula... More Information » « Less Information

Blantyre

11-15 of 709 Reports
Total Reports Avg Reports Per Day % Verified
709 0.45 99.72%