Showing Reports From Feb 17, 2016 to Oct 15, 2019 Change Date Range

Or choose your own date range:

From: To: Go
1-5 of 19 Reports

Kwachepa Chitetezo kuno ku Nankhaka

Categories

Security

Kwachepa Chitetezo kuno ku Nankhaka 0 Verified

11:44 Aug 01, 2018

Kuno kwathu kwa kanthonga, Nankhaka ward khalidwe la akuba likunka nichuluka, mwina chifukwa police nku Lumbadzi ndi Kanengo nde anthu amasibwa... More Information » « Less Information

Lilongwe

Nkhani yakuchepa kwa chitetezo ku Katawa 0 Verified

17:14 Apr 18, 2018

Katawa kuba kwachuluka police sikutithandiza. Komanso magetsi More Information » « Less Information

Mzuzu

Khonsolo itiganizire pa msika wa Malingunde

Categories

Security

Khonsolo itiganizire pa msika wa Malingunde 0 Verified

15:01 Mar 22, 2018

Ine ndati ndipempheko ku khonsolo kuti itikonzere ti migula kapena kuti ngalande zodutsamo madzi pa msika wa Malingunde. Atatikonderanso nkumanga... More Information » « Less Information

Lilongwe

Vuto la Akuba Mchengautuba West

Categories

Security

Vuto la Akuba Mchengautuba West 1 Verified

15:26 Aug 15, 2017

Mchengautuba west akuba akuvuta kwambiri m'maka kwa Belewa sitikudziwa kuti atsogoleri athu malingaliro awo pa nkhani imeneyi ndi otani More Information » « Less Information

Mzuzu, Mzimba, Northern Region, Malawi

Unkhungu ku Mchengautuba west

Categories

Security

Unkhungu ku Mchengautuba west 0 Verified

11:52 Jul 24, 2017

Kuno ku Mchengautuba west unkhungu ngunandi. Community police yuchitapo kanthu yayi More Information » « Less Information

Mzuzu

1-5 of 19 Reports
Total Reports Avg Reports Per Day % Verified
647 0.48 99.69%