Showing Reports From Feb 17, 2016 to Jan 23, 2021 Change Date Range

Or choose your own date range:

From: To: Go
1-5 of 124 Reports

Ngalande za pa msika waukulu wa Kasungu

Categories

WASH

Ngalande za pa msika waukulu wa Kasungu 27 Verified

11:52 Feb 24, 2020

Ngalande za pa msika waukulu wa Kasungu ndi zosafukula zomwe zikuchititsa kuti madzi adzilowa mu msika chonde atithandize More Information » « Less Information

Kasungu

Pempho La Bin Ku Zolozolo 1 Verified

07:31 Feb 22, 2020

Ndati ndipemphe nawo chithandizo choti khonsolo itibweresere bin yayikulu pa msika wa Apostolic. Malowa akubweresa chiophyezo cha matenda chifukwa... More Information » « Less Information

Mzuzu

Kusowa Kwa Ma Toilet Abwino M'misika

Categories

WASH

Kusowa Kwa Ma Toilet Abwino M'misika 1 Verified

07:44 Feb 06, 2020

Kuno ku Kasungu misika yambiri ing'onoing'ono mulibe ma toilet koma ma tiketi timaduladaily. Kodi ndalamazo zimagwira ntchito yanji More Information » « Less Information

Kasungu

Kufunikira kwa Ngalande ku Kasungu

Categories

WASH

Kufunikira kwa Ngalande ku Kasungu 0 Verified

10:48 Feb 05, 2020

Ngalande za mu msika ndi zosafukula kuno ku Kasungu chinthu chomwe chikupangisa kuti madzi azilowa pamalo ogulitsira malonda More Information » « Less Information

Kasungu

Kusatuluka Kwa Madzi

Categories

WASH

Kusatuluka Kwa Madzi 0 Verified

21:15 Jan 20, 2020

Kusatuluka kwa madzi mmalo ena oyandikira pa town assembly kuno ku Kasungu kukweza chiophyeza chakufala kwa matenda odza Kamba ka Ntchetche More Information » « Less Information

Kasungu

1-5 of 124 Reports
Total Reports Avg Reports Per Day % Verified
745 0.41 99.73%