Showing Reports From Feb 17, 2016 to Jan 26, 2021 Change Date Range

Or choose your own date range:

From: To: Go
21-25 of 64 Reports

Tiyamikire Khansala wathu Namiyango Ward

Categories

Other

Tiyamikire Khansala wathu Namiyango Ward 1 Verified

16:59 Jan 25, 2017

Kuno ku Namiyango ndati ndiyamikire Khansala wathu ntchito akugwira bwino limodzi ndi mafumu. pokhala pofunika zokambirana amayitanitsa anthu... More Information » « Less Information

Blantyre, Namiyango

Pempho kwa anthu aku Bangwe Mthandizi

Categories

Other

Pempho kwa anthu aku Bangwe Mthandizi 0 Verified

10:58 Jan 25, 2017

Ndikupempha anthu aku Bangwe Mthandizi ward kuti tatiyeni tonse tigwirane manja pa nkhani za chitukuko posatengera kuti mzanga ndi wa chipani... More Information » « Less Information

Blantyre, Southern Region, Malawi

Ku Chilomoni kwa Nthukwa Msika ukuchepa

Categories

Other

Ku Chilomoni kwa Nthukwa Msika ukuchepa 0 Verified

10:40 Jan 25, 2017

Ife kuno Ku chilomon kwa nthukwa tufuna mutikonzere msika wathu ukuchepa. ine Samuel salema More Information » « Less Information

Blantyre

Tikudikirabe kuno kwa Tsabango

Categories

Other

Tikudikirabe kuno kwa Tsabango 1 Verified

13:51 Jan 11, 2017

Ndati ndidziwitse khansala wathu kuno kwa Tsabango 2 kuti tikudikirabe lonjezo lawo loti adzaitanitsa msonkhano kuti anthu tikakambirane za... More Information » « Less Information

Lilongwe

Expectations on the election of a new Mayor in Blantyre

Categories

Other

Expectations on the election of a new Mayor in Blantyre 0 Verified

09:34 Jan 10, 2017

1. The city council should step up efforts in waste collection. For some areas they should not stick to their program of collecting waste twice... More Information » « Less Information

Blantyre, Southern Region, Malawi

21-25 of 64 Reports
Total Reports Avg Reports Per Day % Verified
745 0.41 99.73%