Verified

Nseu ku kasungu

12:42 Apr 12 2016 Kasungu, Central, Malawi

Description
Nseu wa ku ma puloti suli bwino kukagwa mvula timavutika chifukwa cha matope ma galimoto amavutika kuyenda, nazo njinga sitimayendesa chifuka cha ku telela kwa mu nseu....tinawauza a MP anthu koma anangobweletsa nchenga komano ntchito siyinayambike
Credibility: UP DOWN 0
Leave a Comment
Name:
Email:
Comments:
Security Code:
14 + 8 =

Additional Reports

Pempho pa nkhani ya ma lipoti pa Mzinda

16:03 Nov 06, 2016

Lilongwe, Kauma, 36.87 Kms

Request for a new police unit

14:33 May 11, 2017

Dowa, 39.28 Kms

Kuno ku Dowa vuto ndi kolite ya madzi

13:41 Dec 17, 2016

Dowa, 39.37 Kms

Waste Collection a challenge in Nkhotakota

17:45 Jan 30, 2017

Nkhotakota,, 43.07 Kms

Njinga Za moto

10:26 Dec 06, 2019

Kaomba, Kasungu, 43.76 Kms