Verified

chipatala

09:14 Dec 4 2019 Chibavi east,Mzuzu

chipatala
Description
Chibavi east tili ndi vuto la chipatala,anamanga clinic in 2006 koma mpaka pano ndi under five clinic basi,koma timafuna ikanakhala full clinic ndipo itha kuthandiza anthu aku Chibavi west,Mchengautuwa East and West,and chibanja.

Well wisher watimangila mpanda 2month ago
Credibility: UP DOWN 0
Comments
Mc Donald Gondwe (Dec 5 2019)
Nkhani ya chipatala cha ku Chiwavi tikuyidziwa ndipo department ya zaumoyo, komiti yazaumoyo komanso ma stakeholders ena akuchita chotheka kuti mwina zinthu zisinthe ku Chiwavi pankhani ya zaumoyo. Dela la Chiwavi monga madela ena mmdzinda wa Mzuzu kuli anthu ambiri moti nkofunikadi kuti zipatala zikhale pa pafupi pafupi. Pakali pano, boma likukudza chipatala cha Mapale-Mzuzu Urban Health Centre kuti mwina chithe kufikila anthu ambiri komanso chidzichita provide ma service ambiri a zaumoyo.
Leave a Comment
Name:
Email:
Comments:
Security Code:
20 + 10 =

Additional Reports

Zolozolo Bridge kwa Juma *Resolved*

12:57 Aug 02, 2016

Mzuzu, Zolozolo, 0.3 Kms

PIPE YOPHULIKA *Resolved*

15:01 Aug 05, 2016

Mzuzu, Zolozolo, 0.3 Kms

Sugzo ilo tili nalo kuno ku Masasa

14:32 Nov 19, 2016

MASASA, MZUZU, 0.3 Kms

Kuno ku Masasa Maji ayo tikumwa mbawemi cha

14:57 Nov 19, 2016

Masasa, Mzuzu, 0.3 Kms

Suzgo kuno ku Masasa ni Maji

07:57 Nov 21, 2016

Masasa, Mzuzu, 0.3 Kms