Verified

Vuto la Akuba Mchengautuba West

15:26 Aug 15 2017 Mzuzu, Mzimba, Northern Region, Malawi

Description
Mchengautuba west akuba akuvuta kwambiri m'maka kwa Belewa sitikudziwa kuti atsogoleri athu malingaliro awo pa nkhani imeneyi ndi otani
Credibility: UP DOWN 0
Comments
Denis Moyo (Aug 15 2017)
Nkhani imeneyi taimva. Vuto lilipo ndi lakuti kuchokera pa Chigamulo cha khothi za vakabu ndi povuta kuti community police igwire ntchito yake bwinobwino chifukwa ena mwa anthu omwe angakumane nawo usiku olo akuwaganizira kuti ndi oti atha kupanga za upandu iwo kwapano ali ndi ufulu woyenda nthawi imeneyo. Tingoyesesa kuti tingapange bwanji kuti mwina apolisi azitha kufikira kwathu kuno mwapafupi komanso nthawi ndi nthawi.
Leave a Comment
Name:
Email:
Comments:
Security Code:
12 + 8 =

Additional Reports

Zolozolo Bridge kwa Juma *Resolved*

12:57 Aug 02, 2016

Mzuzu, Zolozolo, 0 Kms

PIPE YOPHULIKA *Resolved*

15:01 Aug 05, 2016

Mzuzu, Zolozolo, 0 Kms

Sugzo ilo tili nalo kuno ku Masasa

14:32 Nov 19, 2016

MASASA, MZUZU, 0 Kms

Kuno ku Masasa Maji ayo tikumwa mbawemi cha

14:57 Nov 19, 2016

Masasa, Mzuzu, 0 Kms

Suzgo kuno ku Masasa ni Maji

07:57 Nov 21, 2016

Masasa, Mzuzu, 0 Kms