Verified

Kuthokoza ndi kupempha pa za msika wa Geisha

12:43 Feb 6 2017 Mzuzu, Northern Region, Malawi

Description
Tikuthokoza kuti malo amsika anatheka ndipo pano anthu ayambapo kugwiritsa ntchito komabe pakufunika kuwathandiza kuti amange ma shop olimba komanso pakhale dongosolo za malo otaya zinyalala
Credibility: UP DOWN 0
Comments
Yona Mkandawire (Feb 6 2017)
Tathokoza chifukwa cha uthenga wanu. Ma plan okonza bwino msika umenewu alipo.
Leave a Comment
Name:
Email:
Comments:
Security Code:
16 + 5 =

Additional Reports

Zolozolo Bridge kwa Juma *Resolved*

12:57 Aug 02, 2016

Mzuzu, Zolozolo, 0 Kms

PIPE YOPHULIKA *Resolved*

15:01 Aug 05, 2016

Mzuzu, Zolozolo, 0 Kms

Sugzo ilo tili nalo kuno ku Masasa

14:32 Nov 19, 2016

MASASA, MZUZU, 0 Kms

Kuno ku Masasa Maji ayo tikumwa mbawemi cha

14:57 Nov 19, 2016

Masasa, Mzuzu, 0 Kms

Suzgo kuno ku Masasa ni Maji

07:57 Nov 21, 2016

Masasa, Mzuzu, 0 Kms