Verified

Pempho pa nkhani ya ma lipoti pa Mzinda

16:03 Nov 6 2016 Lilongwe, Kauma

Description
Amene mukupanga za Mzinda chonde pamene mukutilumikiza ndi atsogoleri komanso ama Bungwe musalowetse ndale likhale loyima palokha Nadine T S Banda. kwa Kauma
Credibility: UP DOWN 1
Comments
Mzinda (Nov 6 2016)
Tathokoza chifukwa chotumiza uthenga umenewu. Zoonadi, Mzinda ukungofuna kulumikiza anthu ndi atsogoleri komanso ama bungwe kotero palibe kupenya za chipani cha munthu kapena komwe akuchokera.
Leave a Comment
Name:
Email:
Comments:
Security Code:
15 + 1 =

Additional Reports

Kuno ku Dowa vuto ndi kolite ya madzi

13:41 Dec 17, 2016

Dowa, 2.52 Kms

Lumbadzi pa Msika Palibe Bin

00:47 Aug 18, 2016

Lilongwe, Malawi, 11.7 Kms

Pempho kuno ku Area 24

09:37 Oct 16, 2016

Lilongwe, Area 24, 13.39 Kms

Magetsi akuvuta kwambiri kuno kwa Chinsapo

11:50 Nov 03, 2016

Lilongwe, Chinsapo, 14.59 Kms

Chitukuko ndi chotheka ngati pali kugwirirzana

15:49 Dec 04, 2016

Lilongwe, Chikulu, 15.83 Kms