Verified

Adziwitseni atsogoleri athu za Mzinda

15:20 Sep 18 2016 Lilongwe North

Description
Kuno ku lilongwe north constituency akhansala athu Bambo Kazamira ati sadadziwitsidwe za Mzinda. Tsono tikatuma uthenga atithandiza bwanji?
Credibility: UP DOWN 0
Comments
Mzinda (Sep 18 2016)
Tathokoza chifukwa cha uthenga wanu. Ndizoonadi sadadziwitsidwe chifukwa kwapanopa tayamba ndi makhansala amu Lilongwe city kaye. komabe m'mene mwatumira uthengawu tiyesetsa kuti uwafikire.
Leave a Comment
Name:
Email:
Comments:
Security Code:
14 + 1 =

Additional Reports

We don't have a hospital

10:21 Apr 13, 2016

Lilongwe, Central Region, Malawi, 0 Kms

Request for Water Kiosk in Chitukula Area

09:28 Sep 02, 2016

Lilongwe, Nankhaka, Malawi, 0 Kms

Tithokoze atikonzera Bridge ya Chiwoko

10:02 Sep 05, 2016

Lilongwe, Central Region, Malawi, 0 Kms

Akhansala athu sanayambe zomwe adalonjeza

17:36 Sep 05, 2016

Lilongwe, Central Region, Malawi, 0 Kms

Nthawi Ya kuzima kwa Magetsi

08:55 Sep 08, 2016

Lilongwe, Area 24, 0 Kms