Verified

Police station yotithandiza kulibe

13:29 Apr 12 2016 Balaka, Southern, Malawi

Description
Kwathu kuno katundu akubedwa.. anthu akuphedwa paliibe chabwino kukacha timamva nkhani za chisoni ........ a MP anthu tinawafotokozela kuti kuta khala police station bola tithandizika....... anangoti amva
Credibility: UP DOWN 0
Comments
Mzinda (Aug 12 2016)
Mutalongosola bwino kuti ku Balaka dera la pati kuti muthe kuthandizika mwachangu.
Leave a Comment
Name:
Email:
Comments:
Security Code:
11 + 8 =

Additional Reports

Water is a big problem

10:04 Apr 13, 2016

Liwonde, Southern, Malawi, 31.66 Kms

Pempho kuno ku Lizulu Ntcheu

17:10 Nov 27, 2016

Ntcheu, Central Region, Malawi, 39.31 Kms

Bridge yinakokoloka

13:12 Apr 12, 2016

Zomba, Southern, Malawi, 49.48 Kms

Blackouts in Zomba

13:20 Nov 24, 2016

Zomba, 56.48 Kms

Vutu lakuzima kwa magetsi

07:28 Jan 28, 2017

Zomba, 57.55 Kms