Showing Reports From Feb 17, 2016 to Mar 19, 2019 Change Date Range

Or choose your own date range:

From: To: Go
1-5 of 601 Reports

Good Insights on Council Operations 4709 Verified

17:51 Sep 02, 2018

Let me commend the panelists on today's program for sharing information that I think others like me surely appreciate how the council works... More Information » « Less Information

Blantyre

Vuto Lakusiyasiya Kwa Madzi

Categories

Water

Vuto Lakusiyasiya Kwa Madzi 6 Verified

15:13 Aug 31, 2018

Kuno ku Mbayani limodzi mwa mavuto omwe tili nawo ndi kusiyasiya kwa madzi. Ndine Maggie Chirwa More Information » « Less Information

Blantyre

Alimbikitse Ukhondo Kuno Kwa Kauma 1 Verified

15:02 Aug 31, 2018

Ndati ndifikire ndi uthenga kwa Khansala wathu ndinso mafumu kuno ku Nyama ward kwa Kauma kuti achitepo kanthu pa khalidwe la anthu omwe amaunjika... More Information » « Less Information

Lilongwe

Pipe Ya Madzi Yaphulika *Resolved*

Categories

Water

Pipe Ya Madzi Yaphulika *Resolved* 1 Verified

15:12 Aug 28, 2018

Uthenga ufike ku wota board pipe yaphulika nkati mwa msika wa lizulu. Ku ntunda mmunsi mwa bank ya standard. More Information » « Less Information

Lilongwe

Pa Zokambirana Za Miseu

Categories

Roads

Pa Zokambirana Za Miseu 0 Verified

18:38 Aug 26, 2018

Ine ndati ndithirepo ndemanga program ya lero. Zoonadi ndibwino anthu tiziziwa chonchi kuti kodi ma contractor amasankhidwa bwnanji. Zitha kukhala... More Information » « Less Information

Blantyre

1-5 of 601 Reports
Total Reports Avg Reports Per Day % Verified
601 0.53 99.67%